Home 2

Alimi ang’onoang’ono awalimbikitsa kumagwiritsa ntchito zipangizo zopezekeratu m’madera awo ngati akufuna kuthana ndi mavuto a kuchepa kwa zokolora. A Christopher Nkhoma, mulangizi wa mkulu wa dera la ulimi la …