Alimi ang’onoang’ono awalimbikitsa kugwiritsa ntchito manyowa a mbeya.
Alimi ang’onoang’ono awalimbikitsa kumagwiritsa ntchito zipangizo zopezekeratu m’madera awo ngati akufuna kuthana ndi mavuto a kuchepa kwa zokolora. A Christopher Nkhoma, mulangizi…